Genesis 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuyambira lero ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, akhala anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga ngati mmene alili Rubeni ndi Simiyoni.+
5 Kuyambira lero ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, akhala anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga ngati mmene alili Rubeni ndi Simiyoni.+