Genesis 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena za ine, pamene ndinkachokera ku Padani, mayi ako Rakele anandifera+ panjira mʼdziko la Kanani, patatsala mtunda ndithu kuti tifike ku Efurata.+ Zitatero, ndinawaika mʼmanda panjira yopita ku Efurata, kapena kuti Betelehemu.”+
7 Kunena za ine, pamene ndinkachokera ku Padani, mayi ako Rakele anandifera+ panjira mʼdziko la Kanani, patatsala mtunda ndithu kuti tifike ku Efurata.+ Zitatero, ndinawaika mʼmanda panjira yopita ku Efurata, kapena kuti Betelehemu.”+