-
Genesis 48:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Maso a Isiraeli anali atafooka chifukwa chokalamba, moti sankatha kuona. Yosefe anabweretsa anawo pafupi ndi bambo ake, ndipo bambo akewo anakisa anawo nʼkuwakumbatira.
-