Genesis 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anadalitsa Yosefe kuti:+ “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala mʼbusa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+
15 Kenako anadalitsa Yosefe kuti:+ “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala mʼbusa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+