Genesis 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Anawa azidziwika ndi dzina langa komanso mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki,Anawa adzachulukane nʼkukhala gulu la anthu ambiri padziko lapansi.”+
16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Anawa azidziwika ndi dzina langa komanso mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki,Anawa adzachulukane nʼkukhala gulu la anthu ambiri padziko lapansi.”+