Genesis 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma sudzakhala wapamwamba kuposa abale ako, chifukwa mofanana ndi madzi osefukira unalephera kudziletsa, ndipo unakwera pogona pa bambo ako.+ Pa nthawiyo unadetsa* bedi langa. Anagonapo ndithu ameneyu!
4 Koma sudzakhala wapamwamba kuposa abale ako, chifukwa mofanana ndi madzi osefukira unalephera kudziletsa, ndipo unakwera pogona pa bambo ako.+ Pa nthawiyo unadetsa* bedi langa. Anagonapo ndithu ameneyu!