Genesis 49:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe moyo wanga, usakhale nawo pagulu lawo. Iwe mtima wanga,* usagwirizane ndi mpingo wawo, chifukwa atakwiya anapha anthu,+ ndipo anapundula* ngʼombe zamphongo pofuna kusangalala.
6 Iwe moyo wanga, usakhale nawo pagulu lawo. Iwe mtima wanga,* usagwirizane ndi mpingo wawo, chifukwa atakwiya anapha anthu,+ ndipo anapundula* ngʼombe zamphongo pofuna kusangalala.