Genesis 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkwiyo wawo ukhale wotembereredwa chifukwa ndi wankhanza, komanso ukali wawo chifukwa umachita zinthu mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:7 Galamukani!,9/8/1987, tsa. 24
7 Mkwiyo wawo ukhale wotembereredwa chifukwa ndi wankhanza, komanso ukali wawo chifukwa umachita zinthu mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+