Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pakhosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakuweramira.+
8 Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pakhosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakuweramira.+