Genesis 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Mwana wanga, ukadzadya nyama imene wapha udzachokapo. Iye wapinda mawondo ake nʼkudziwongola ngati mkango umene wagona pansi. Ndipo mofanana ndi mkango, ndi ndani amene angamudzutse? Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 83-84
9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Mwana wanga, ukadzadya nyama imene wapha udzachokapo. Iye wapinda mawondo ake nʼkudziwongola ngati mkango umene wagona pansi. Ndipo mofanana ndi mkango, ndi ndani amene angamudzutse?