-
Genesis 49:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Atamanga bulu wake pamtengo wa mpesa ndi kamwana ka bulu wake pamtengo wa mpesa wabwino, adzachapa zovala zake muvinyo komanso malaya ake mʼmadzi ofiira a mphesa.
-