Genesis 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zebuloni+ adzakhala mʼmbali mwa nyanja, adzakhala pafupi ndi doko pamene pamaima sitima.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+
13 Zebuloni+ adzakhala mʼmbali mwa nyanja, adzakhala pafupi ndi doko pamene pamaima sitima.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+