Genesis 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba. Amagona pansi kuti apume, atanyamula matumba awiri a katundu.