Genesis 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dani adzakhala njoka yobisala mʼmbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala mʼmphepete mwa njira, imene imaluma zidendene za hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+
17 Dani adzakhala njoka yobisala mʼmbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala mʼmphepete mwa njira, imene imaluma zidendene za hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+