Genesis 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yosefe+ ndi mphukira yamtengo wobala zipatso. Iye ndi mtengo wobala zipatso pakasupe, umene nthambi zake zimafika pamwamba pa khoma la mpanda.
22 Yosefe+ ndi mphukira yamtengo wobala zipatso. Iye ndi mtengo wobala zipatso pakasupe, umene nthambi zake zimafika pamwamba pa khoma la mpanda.