Genesis 49:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake,+ ndipo manja ake anakhalabe amphamvu ndi ochenjera.+ Zimenezi zinachokera mʼmanja mwa wamphamvu wa Yakobo, zinachokera kwa mʼbusa, mwala wa Isiraeli.
24 Koma uta wake unakhalabe pamalo ake,+ ndipo manja ake anakhalabe amphamvu ndi ochenjera.+ Zimenezi zinachokera mʼmanja mwa wamphamvu wa Yakobo, zinachokera kwa mʼbusa, mwala wa Isiraeli.