Genesis 49:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye* ndi wochokera kwa Mulungu wa bambo ako ndipo adzakuthandiza. Iye ali ndi Wamphamvuyonse, ndipo Mulunguyo adzakudalitsa pokupatsa madzi ochokera kumwamba ndi pansi pa nthaka.+ Adzakudalitsa pokupatsa ana ndi ziweto zambiri.*
25 Iye* ndi wochokera kwa Mulungu wa bambo ako ndipo adzakuthandiza. Iye ali ndi Wamphamvuyonse, ndipo Mulunguyo adzakudalitsa pokupatsa madzi ochokera kumwamba ndi pansi pa nthaka.+ Adzakudalitsa pokupatsa ana ndi ziweto zambiri.*