Genesis 49:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Madalitso a bambo ako adzaposa madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale. Adzaposanso zinthu zosiririka za zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzapitiriza kukhala pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+
26 Madalitso a bambo ako adzaposa madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale. Adzaposanso zinthu zosiririka za zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzapitiriza kukhala pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+