Genesis 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,3/2014, tsa. 7 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, tsa. 61/1/2004, ptsa. 28-29
16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+
1:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,3/2014, tsa. 7 Nsanja ya Olonda,2/15/2007, tsa. 61/1/2004, ptsa. 28-29