Genesis 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Benjamini+ adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ Mʼmawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zinthu zimene watenga atagonjetsa adani ake.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:27 Tsanzirani, tsa. 142 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 29
27 Benjamini+ adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ Mʼmawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zinthu zimene watenga atagonjetsa adani ake.”+