Genesis 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Onsewa ndi mafuko 12 a Isiraeli, ndipo zimenezi ndi zimene bambo awo anawauza pamene ankawadalitsa. Aliyense anamupatsa madalitso omuyenerera.+
28 Onsewa ndi mafuko 12 a Isiraeli, ndipo zimenezi ndi zimene bambo awo anawauza pamene ankawadalitsa. Aliyense anamupatsa madalitso omuyenerera.+