Genesis 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Yosefe analamula atumiki ake omwe anali madokotala, kuti akonze mtembo wa bambo ake ndi mankhwala kuti usawonongeke.+ Choncho madokotalawo anakonza mtembo wa Isiraeli. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2002, ptsa. 29-30
2 Kenako Yosefe analamula atumiki ake omwe anali madokotala, kuti akonze mtembo wa bambo ake ndi mankhwala kuti usawonongeke.+ Choncho madokotalawo anakonza mtembo wa Isiraeli.