Genesis 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Bambo anga anandilumbiritsa+ kuti: “Inetu ndikufa.+ Ukandiike mʼmanda amene ndinakonza+ mʼphanga kudziko la Kanani.”+ Ndiye chonde, ndiloleni ndipite ndikaike bambo anga, pambuyo pake ndikabweranso.’”
5 ‘Bambo anga anandilumbiritsa+ kuti: “Inetu ndikufa.+ Ukandiike mʼmanda amene ndinakonza+ mʼphanga kudziko la Kanani.”+ Ndiye chonde, ndiloleni ndipite ndikaike bambo anga, pambuyo pake ndikabweranso.’”