Genesis 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu onse amʼnyumba ya Yosefe, abale ake, ndi anthu amʼnyumba ya bambo ake, anapita naye limodzi.+ Ku Goseni kunangotsala ana awo aangʼono, nkhosa, mbuzi ndi ngʼombe zawo.
8 Anthu onse amʼnyumba ya Yosefe, abale ake, ndi anthu amʼnyumba ya bambo ake, anapita naye limodzi.+ Ku Goseni kunangotsala ana awo aangʼono, nkhosa, mbuzi ndi ngʼombe zawo.