Genesis 50:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akanani amene ankakhala mʼdzikolo anaona anthuwo akulira pamalo opunthira mbewu a Atadi, ndipo anati: “Aiguputowa ali pa chisoni chachikulu kwambiri!” Nʼchifukwa chake malowo anawatchula kuti Abele-miziraimu,* ndipo ali mʼchigawo cha Yorodano.
11 Akanani amene ankakhala mʼdzikolo anaona anthuwo akulira pamalo opunthira mbewu a Atadi, ndipo anati: “Aiguputowa ali pa chisoni chachikulu kwambiri!” Nʼchifukwa chake malowo anawatchula kuti Abele-miziraimu,* ndipo ali mʼchigawo cha Yorodano.