Genesis 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uchipange chonchi: Mulitali chikhale mamita 134,* mulifupi mamita 22, ndipo kutalika kwake kuyambira pansi mpaka pamwamba chikhale mamita 13. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:15 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Galamukani!,1/2007, ptsa. 20-212/8/1997, tsa. 19
15 Uchipange chonchi: Mulitali chikhale mamita 134,* mulifupi mamita 22, ndipo kutalika kwake kuyambira pansi mpaka pamwamba chikhale mamita 13.