-
Genesis 50:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 ‘Mukamuuze Yosefe kuti: “Mwana wanga, zimene abale ako anakuchitira si zabwino. Koma ndikukupempha kuti uwakhululukire zonse zimene anakuchitira.”’ Ndiye chonde, tikhululukireni ife akapolo a Mulungu wa bambo anu.” Atamuuza zimenezi, Yosefe analira kwambiri.
-