Genesis 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako abale akewonso anafika nʼkudzigwetsa pansi pamaso pake, ndipo ananena kuti: “Tikudzipereka kwa inu ngati akapolo anu.”+
18 Kenako abale akewonso anafika nʼkudzigwetsa pansi pamaso pake, ndipo ananena kuti: “Tikudzipereka kwa inu ngati akapolo anu.”+