Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu+ amʼbadwo wachitatu. Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamawondo a Yosefe.* Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:23 Nsanja ya Olonda,9/15/1995, ptsa. 20-21
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu+ amʼbadwo wachitatu. Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamawondo a Yosefe.*