Genesis 50:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakuthandizani+ ndipo adzakutulutsani ndithu mʼdziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analumbira kuti adzalipereka kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+
24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakuthandizani+ ndipo adzakutulutsani ndithu mʼdziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analumbira kuti adzalipereka kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+