Genesis 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo, nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+
20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo, nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+