Genesis 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa mʼchingalawacho, iwe ndi banja lako, chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa mʼbadwo uwu.+
7 Kenako Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa mʼchingalawacho, iwe ndi banja lako, chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa mʼbadwo uwu.+