Genesis 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 311/1/2004, tsa. 29
2 Pa nyama zosadetsedwa zamtundu uliwonse utengepo zokwanira 7,*+ yaimuna ndi yaikazi yake. Koma pa nyama zodetsedwa zilizonse utengepo ziwiri zokha, yaimuna ndi yaikazi yake.