Genesis 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kwangotsala masiku 7 okha kuti ndigwetse chimvula+ padziko lapansi kwa masiku 40, masana ndi usiku.+ Ndipo ndidzaseseratu padziko lapansi chamoyo chilichonse chimene ndinachipanga.”+
4 Kwangotsala masiku 7 okha kuti ndigwetse chimvula+ padziko lapansi kwa masiku 40, masana ndi usiku.+ Ndipo ndidzaseseratu padziko lapansi chamoyo chilichonse chimene ndinachipanga.”+