Genesis 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho chigumulacho chisanayambe, Nowa analowa mʼchingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake ndi akazi a ana ake.+
7 Choncho chigumulacho chisanayambe, Nowa analowa mʼchingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake ndi akazi a ana ake.+