Genesis 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo analowa limodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse, nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* zapadziko lapansi zamtundu uliwonse, zamoyo zouluka zamtundu uliwonse, mbalame zilizonse ndiponso zamoyo zilizonse zamapiko.
14 Iwo analowa limodzi ndi nyama zakutchire zamtundu uliwonse, nyama zoweta zamtundu uliwonse, nyama zokwawa* zapadziko lapansi zamtundu uliwonse, zamoyo zouluka zamtundu uliwonse, mbalame zilizonse ndiponso zamoyo zilizonse zamapiko.