Genesis 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zamoyo zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tingʼonotingʼono toyenda mʼmagulu, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+
21 Choncho zamoyo zonse zoyenda padziko lapansi, monga zamoyo zouluka, nyama zoweta, nyama zakutchire, ndiponso tizilombo tonse tingʼonotingʼono toyenda mʼmagulu, zinafa+ pamodzi ndi anthu onse.+