Genesis 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anakumbukira Nowa ndi nyama zonse zakutchire ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo mʼchingalawa chija.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa kuti chimphepo chiwombe padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.
8 Koma Mulungu anakumbukira Nowa ndi nyama zonse zakutchire ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo mʼchingalawa chija.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa kuti chimphepo chiwombe padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.