-
Genesis 8:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 ndipo anatumiza khwangwala. Choncho khwangwalayo ankangouluka kunja nʼkumabwerera kuchingalawacho mpaka madzi ataphwa padziko lapansi.
-