Genesis 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma njiwayo sinapeze malo alionse oti nʼkuterapo. Choncho, inabwerera kwa iye mʼchingalawamo chifukwa madzi anali asanaphwe padziko lonse lapansi.+ Itabwerera, iye anatulutsa dzanja lake, nʼkuitenga ndipo anailowetsa mʼchingalawamo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Nsanja ya Olonda,1/15/1992, tsa. 31
9 Koma njiwayo sinapeze malo alionse oti nʼkuterapo. Choncho, inabwerera kwa iye mʼchingalawamo chifukwa madzi anali asanaphwe padziko lonse lapansi.+ Itabwerera, iye anatulutsa dzanja lake, nʼkuitenga ndipo anailowetsa mʼchingalawamo.