Genesis 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mʼchaka cha 601 cha Nowa,+ mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, madzi anali ataphwa padziko lapansi. Nowa anatsegula chibowo chimene chinali padenga la chingalawacho nʼkuyangʼana kunja ndipo anaona kuti nthaka yayamba kuuma. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Nsanja ya Olonda,8/1/2013, tsa. 145/15/2003, tsa. 5
13 Tsopano mʼchaka cha 601 cha Nowa,+ mʼmwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo, madzi anali ataphwa padziko lapansi. Nowa anatsegula chibowo chimene chinali padenga la chingalawacho nʼkuyangʼana kunja ndipo anaona kuti nthaka yayamba kuuma.