Genesis 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso, zamoyo zilizonse, nyama zilizonse zokwawa, zamoyo zouluka zilizonse, chilichonse chimene chimayenda padziko lapansi, zinatuluka mʼchingalawamo monga mwa magulu awo.+
19 Komanso, zamoyo zilizonse, nyama zilizonse zokwawa, zamoyo zouluka zilizonse, chilichonse chimene chimayenda padziko lapansi, zinatuluka mʼchingalawamo monga mwa magulu awo.+