10 Ndikuchitanso panganoli ndi chamoyo chamtundu uliwonse chimene muli nacho limodzi, monga mbalame, zinyama komanso zamoyo zonse zapadziko lapansi, kutanthauza zonse zimene zinatuluka mʼchingalawa, kapena kuti chamoyo chilichonse chapadziko lapansi.+