Genesis 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pangano limene ndikuchita nanu ndi ili: Zamoyo zonse sizidzawonongedwanso ndi chigumula, ndipo chigumula sichidzachitikanso nʼkuwononga dziko lapansi.”+
11 Pangano limene ndikuchita nanu ndi ili: Zamoyo zonse sizidzawonongedwanso ndi chigumula, ndipo chigumula sichidzachitikanso nʼkuwononga dziko lapansi.”+