-
Genesis 9:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Atamva zimenezo, Semu ndi Yafeti anatenga chofunda nʼkuchiika pamapewa awo ndipo anayenda chafutambuyo. Atalowa mutentimo, anafunditsa bambo awo nʼkuwabisa maliseche, iwo akuyangʼana kumbali moti sanaone maliseche a bambo awo.
-