Genesis 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iyi ndi mbiri ya ana a Nowa, omwe ndi Semu,+ Hamu ndi Yafeti. Iwowa anabereka ana pambuyo pa Chigumula.+
10 Iyi ndi mbiri ya ana a Nowa, omwe ndi Semu,+ Hamu ndi Yafeti. Iwowa anabereka ana pambuyo pa Chigumula.+