-
Genesis 1:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho Mulungu anapanga nyama zakutchire monga mwa mitundu yake komanso nyama zoweta monga mwa mitundu yake. Anapanganso nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yake. Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.
-