-
Genesis 10:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iye anakhala mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova. Nʼchifukwa chake pali mawu akuti: “Monga Nimurodi mlenje wamphamvu wotsutsa Yehova.”
-