Genesis 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+