Genesis 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anthuwo ankalowera chakumʼmawa, anapeza chigwa mʼdera la Sinara+ ndipo anayamba kukhala kumeneko.
2 Pamene anthuwo ankalowera chakumʼmawa, anapeza chigwa mʼdera la Sinara+ ndipo anayamba kukhala kumeneko.